Messages
Topic:
I've forgotten chichewa!
I'm malawian! born and bred!
until the age of nine i was living in malawi but something happened and i had to move to england and live with my aunti!
it's been like 6 years and in those years i have forgotten how to make sense of it all!
and it's so frustrating that i've lost it and is there anyone who can help me remeber?
Sep 14, 2007
1:26 PM
hahahaha!ama start by saying muli bwanji love
Sep 16, 2007
5:17 PM
U FOR REAL?????
Oct 2, 2007
8:27 AM
AAAHHahaha!!!... napepe phiri, inenso ndi na choka ndilindi zaka 5 koma ndi mamva ndi ku yankulanso..mwina u bwelele ku muzi uzi weta mbuzi. If u,re that fine in person then consider this u're first lesson.
Oct 21, 2007
7:40 AM
mboni yako ndani kuti unaiwala? hahahahahahhhh.. ukuteta amwana....
Oct 30, 2007
5:37 AM
ndifunsireko ndiwe? eh! kaya I LOVE MY LANGUAGE.
Nov 4, 2007
10:06 AM
komatu abale zinazi ndikufuna kuyesana.. tsopano ife helping her rememberyo tikamupangila kuti... angobwerera kaye ku malawi mwina. hahhah
Nov 4, 2007
10:33 PM
Grace, osavutika nazo zimenezi, apite kuti? ameneyu si m`malawiso ndi BLACK BRITISH now, enafe timadyadira MALAWI wathu wabwino, kaya kwa yense wokomedwa ndi chilakhulo chachilendo. MBITE!!!!!!!!!!!!.
Nov 5, 2007
5:39 AM
changa ndingoti ndi chisonitu tosho, moti panopanso mawu andithera.
Nov 6, 2007
3:01 AM
zimenezi ndi zija timati zokanika, kulephera, ah! zadama basi.
Nov 6, 2007
5:32 AM